Focus For Development FFD
social economic development organisation focusing on both empowerment and development!
10/06/2026
Activism that bears results
https://www.facebook.com/share/18sRRP9RqM/
26/05/2026
https://www.facebook.com/100081330802581/posts/1053078220746528/?app=fbl
Akuluakulu amene akukonza mwambo wolimbikitsa chikhalidwe cha amang’anja m'boma la Chikwawa apempha anthu akufuna kwabwino komanso mabungwe kuti awathandize ndi ndalama kuti zizakometse mwambowu.
M'modzi mwa omwe akukonza mwambowu, a Anganile Ngosi, ati mwambowu awukonza kuti alimbitse chikhalidwe cha a Mang'anja komanso Asena ndi zikhulupiliro zawo.
Iwo ati pamwambowu padzakhala zochitika zosiyanasiyana zizawaphunzitse anthuwa kudziwa kuyipa kotengera malamulo m'manja komanso kaganizidwe kangwiro.
A Ngosi ati mwambo wa Chikwawa Cultural Festival, umachitika chaka chilichonse ndipo umalimbikisa chikhalidwe komanso kupereka mwayi kwa achinyamata kuonesa luso losiyanasiyana lomwe alinalo.
Wolemba: Hamidah Kazembe, Chikwawa
05/05/2026
Zathu izi
04/05/2026
04/05/2026
25/02/2026
Calling For Volunteers!
Click here to claim your Sponsored Listing.
Telephone
Website
Address
Chikwawa
05/05/2026
04/05/2026