Kwesh
Artist 🇲🇼 | Life Coach | Film Director 🎥 | The Dopest Media Guy ♠️🔥 | Reels Creator 📸
Nyimbo Koma zimenezi osati Ma phuzo anu mukumayimba Aja achina Lil Al🤣🤣🤣
Akut ma lyric anamuthela pano wathawila ku Chiyao🤣🤣 Skrizzy sudzatheka🤣🙌
31/03/2026
Let’s Drop Feat Bøi Sticx🔥
Kwakwana! It’s a Hit Song🔥
Feat Lil Al and Boi Sticx 🎙️🔥
25/02/2026
Ma Baddie ndi onse bola ku checker Quality😅
20/02/2026
Lil Al Ase Ukudziwa chani Pali anthu ena anangodalitsika olo atakhala zaka 10 osatulitsa track koma day imene akuza dropa track imakhala hit and Iweyo umangomupanga hate Hyphen Chifukwa ndi dolo Komaso Lil Al ndiwe kape Ase..
31/01/2026
Congratulations my bro! Lil Al chomwe ndinkadziwa ndichakut Iweyo sungakhale mu Mario bros (Aba’le) Zomwe ndinkafuna ndizimenezi, pawekha ndiwe dolo Ase ena Aja amangokutayitsa nthawi🔥🔥🔥
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when Kwesh posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.