Jay massivee
NEW AN ARTIST FROM SALIMA 🐘 Bad or Good I sing about Love, Money, S*x and peace.
Zazikulu sizithamanga zimayenda slow.
Welcome to Malawi where Musandiuze means tell me more😩🙌😂
Chinthu chochipeza usakufuna nthawi zambili chimakhala chabwino
06/08/2026
MUSIC RULES
Tikuyamba motele👇
Osamayimba nyimbo ngati wakunja peka komaso kuimba nyimbo yoti a Malawi anvele zimene ukunena, ukhale ndi signature yako yako, Anthu akanva nyimbo azidziwa kuti nyimbo iyi ndi ya adha aja or kuli koti wina wakopa
Apa sitikunena style
Tikunena za kanvekedwe
Kumanveka za wekha osati kunveka ngati Omah lay kapena Wizkid or Diamond platinumz ayi, Do something what people can recognize you easily.
Thank you❤️💜🐘🙏
Nyimbo 5 za masiku ano imakhala imodzi kale, tidasungunula😂😂🙌
Pano tiyamba kuwuzana komaso kugawana malamulo ndi malangizo a nyimbo
Enawa adabadwa koti mpamba ulipo kale pamene iwe ukuyambila pa one osanyanyala😅🏃♂️
Nyimbo za AI zumabhowa kwambiri, zilibe originality.
Kufunika kugula chikwanje😅
Kwada ndisowe ntendere😭
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Address
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when Jay massivee posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.