ADAM
UPCOMING GOSPEL ARTIST๐๐
Follow my page, Phunzirani kuchokera kwa ine, inenso ndiphunzire kuchokera kwa inu .
Opephera akalakwisa ๐ป ๐ข koma osapephera๐
inu ndi nyali yapamwamba pa phiri imene aliyense amayiwona ndipo ikadzimaso anthu amawona
Pakamwa panupo kumapagwira hiya! ๐๐
Taponyani photo ya Amai anu tiwawone, Mother`s Day
Big shout out to my newest top fans! John Butawo, Petersen Makwera, Joseph Yuda
11/10/2025
Umu ndimmene zathera๐๐
Ndani andijoyine tikafuwuule uchi๐๐๐๐
Akati "Zati chani" inu mumayankha kuti chani?โโ๐๐๐
09/10/2025
Short story๐๐
Kodi mukadali mmoyo omwe uja onyengereredwa ndi satana Kumakukopani kuti muchite choyipa?
01/10/2025
Tiwonereko nyimbo iyi masana ano tha https://youtu.be/5W-8gNtnTYY?si=ba9MJjCer3qX1hxa
Download Osayiwala kupanga share
KHAMA KHWILIRO ZIWONETSERENI Feat. Apostle King James Phiri (VISUALISER ) DIR VJ KEN
If you feel down, always remember that for as long as your heart is still beating, you still have a purpose in this life. Have a nice Day.
Click here to claim your Sponsored Listing.