Prove cee
Jus vien mw
03/07/2026
News ππππ
Malipoti ak*ti mnyamata odziwika bwino pa masamba amchezo a tiktok komanso facebook otchedwa Bolo Young watisiya.
Izi ndi malingana ndi zonwe best friend wake Kho khoxy kalilombe walemba pa tsamba lake la Facebook usiku uno.
Bolo Young ndi malemu Malu Malu adachita ngozi sabata latha m'dziko la South Africa.
Malawi wataya mnyamata wodziwa kucheza π moyo suyenda momwe tikuganizila tikusowa ππππ
Mzimu wa Bolo Young ukause mu mtendere.follows
11/06/2026
kodi wikise amaganiza bwanji. eti akuoneka ngati thakathi waxy kay ?
08/06/2026
08/06/2026
Ma edit kumalawi aaah sizinafike apa guys
01/06/2026
ndi angat amene style yakusanalasani
πππ
01/06/2026
Breaking news,,,
Aidfest wayankhula mozembela Gwamba k*ti ngakhale amuika ngati bonus pama artist okayimba ku show ya Gwamba koma iyi sangapange POST poster ya show ku page kwake chifukwa this is fake love chifukwa wamuika pa list yama artist after people reaction,,,,
Kodi inu mukuona k*ti zomwe walankhula Aidfest walakwisa ?
01/06/2026
mwaonela kale nyimbo imeneyi πππ Following page
01/06/2026
Alise amakhala ndi khumbo lake mbali yanu mukukhumba chan apa? Following
29/04/2026
akupeleka mon kwa nonse amalawi ak*t mudikile akakula azkuyendelan nonse komaso ali ndi nyimbo yomwe ituluke posachedwapa tereza tex pangan follow k*t muzathe kuvela nawo luso lamwanayi
29/04/2026
potengera k*ti iye ndi silikali anasakha k*ti chilichose chomwe chili nyumba mwake chizikhala chofanana ndi ntchito yake nakha munthu okuba amasakha chani choti chizifanana ndi ntchito yakeπππ€£π€£
Click here to claim your Sponsored Listing.