CalmTech
secondary tutorials basically in our local language and other computer related tutorials
How to improve network strength in our phones
04/03/2026
Hello guys it's CalmTech again,
Kodi mumadxiwa kuti M***a kupanga. Combine ma pdf files ambirimbiri into one file ?
Kwa ma student anxanga this is very helpful make kumapeto Kwa semester ija , kungotenga ma lecture onse kuika kukhala file imodxi Kuma phanda
Omwe tikufuna video kuti tipange , put you comment osaiwala kupanga follow and share .
Thanks ๐
how to create another account on your phone
27/02/2026
kodi mumadziwa kuti pa phone panupo m***a kukhala ndi ma account opitilira imodxi, ? ๐ค๐ค๐ค
kwa anthu omwe mumabwerekana phone aliyense atha kukhala ndi account yake ndipo aliyense kumapanga install ma application ake kukhala ndizochitika zakekumemeko
next video tifotokoza za mene tingapangire zimezi
please follow and like this page
"together we unit divided we fall"
how to retrieve forgotten password for all websites we logged in before
how to block p**n sites in our phone
make your phone safe for your children ๐
how to retrieve forgotten password?
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Zomba