Mechanic programs

Mechanic programs

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mechanic programs, Automotive, aircraft & boat, 2057 Nancholi, Ginnery Corner.

26/01/2024

Guyz Pali minibus yogulisa 2L if U interested Halla mi #0995911642

11/12/2023

Guyz Galimoto ikakhala Kuti pa flat ukayika gear 1 ukuyenda bho bho pullingso ya bho Koma ukamakwera ntunda ndi gear one ikumazima chimozmozso magear onse kupatulapo reverse

Mukuganiza Kuti Vuto kumakhala chani 🤔

12/09/2023

1rz ukayika gear 1 akamapanga ma jecking mukuganiza k*t chimakhala chili Chan tiyen nazon

02/09/2023

Guyz ndkakumana ndi crash was cable ma gear sakulowa Koma cable ili bho nditan apa

19/08/2023

Guyz Pali corolla engine 7A inapangidwa mode kuchoka Ku automatic kubwera Ki manual

Ikumazima ukayika gear 1 k*t inyamuke Kodi Vuto ndi chani?

23/01/2023

Guyz tyming ya 4A ndi 5A imakhala yofana.???

23/12/2022

GUYZ Nissan tiida ikupanga zopoila

Ukaipaisa moto ili pa parking ikumatheka

Koma ukalowesa gear aliyese
Perdo ikumafika pansi kenaka ikumakwerA wez wez pankana moto kubwerano.

Mwachidule tikhoza kungoti ikuchedwa kubweresa moto ukamaponda Xretor

Chingayambise Ximenez ndi cHaN

26/11/2022

Kodi galimoto tinga iziwe motani k*ti crank shaft ndiyopalika pamene galimoto ikulira????

18/10/2022

Pano tapanga create grouyi pa wapp koma sorry chifukwa panali zopinga zina ndye tachedwa kufoma ndihaleni pa wapp # 0995911642

05/09/2022

Guyz we need to form a group in whatsup about MECHANIC PROGRAM
so of u interested drop your #

Want your business to be the top-listed Autos & Automotive Service in Ginnery Corner?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


2057 Nancholi
Ginnery Corner