Precious Electronics
Want to buy a Phone? WhatsApp 0891562857. Precious Electronics sells electronics products from phones and computers to rice cookers and refrigerators.
Instead of “Okay Cool” admin wayamkha customer kuti “Ok Fool”.
Muthandizeni kupepesa 🙏
03/09/2026
OnePlus 15 0891 56 28 57
03/09/2026
Koma ilipo Foni yoposa iyi padziko pano? Admin wakaika 📞0980641444 0891 56 28 57
03/09/2026
Line up mbambande 🔥
Redmi 15C alipo kuno 📞0980641444 0891 56 28 57
03/09/2026
Osachita manyazi apangeni Tag a Blesser anuwo adziwe kuti mumawanyadira 😃
iPhone 18 ikubwera week yamaya nde adziwiretu kuti kuno atha kuyipeza.
03/09/2026
‼️Mtengo wa foni iyi tatsitsa kwambiri. Zatengeni yanu asanathe‼️
📞0980641444 0891 56 28 57
03/09/2026
✅LayBy
✅2 months
📞0980641444 0891 56 28 57
03/09/2026
Abambo kunyumba akafuna kudyera beans🫘 mwadzidzidzi m***a kuzitereka umu 15 minutes yokha basi zimakhara zapsa kale‼️
Tipezeni mugule chanu 📞0980641444 0891 56 28 57
03/09/2026
Ali ready ndani pano akatisiyire phone ku South Sudan?
02/09/2026
Samsung S20 Ultra, 256GB 🔥📞0980641444 0891 56 28 57
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Address
Guoji Shopping Mall Area 49, Shop C13B
Lilongwe