Nitrix Matama
Official Page of Nitrix Matama |
a Malawian Rapper π²πΌπ²πΌπ²πΌ| Songwriter | Multiple Award Winner koma kumaloto eti Artist
19/06/2026
Rest in peace Ras Kasengwa π ποΈ
Ushasha wa Mind anayamwila kwaine
Check mu comment box
16/06/2026
Page iyi imkandinyoza nde ndaisowetsa
Amene mumanyozedwa muma page muzindipeza ndimasowetsa zimenezi
15/06/2026
DJ BROWN the LOYAL HUSTLE management CEO is set to announce that Loyal hustle studio pano ikupezeka ku area 23 Midland ndipo Mitengo yatsitsidwa nd cholinga chopeleka mwayi kwa oyimba ochepekedwa.
Other important offers,
1. Video + Audio production training kwa onse omwe kufuna kuphunzira production
2. Page monetisation and all platforms (pangan ndalama nd luso)
3. Opening an account on various distributors _(nyimbo zanu zikhale pa Spotify nd ma platforms ose)_
4. Nd zina zambiri zokhudza nyimbo
Contacts
0999848912
0888648439
Buxy Mw uja ndi starπ₯π₯π₯
Link mu comment section
08/06/2026
Kundilanda BREAD kundipasa MBATATA sindimanyumwa takulira zomwezi π₯π₯
ZINJI wa Police kuno π
Link mu comment box
07/06/2026
Her: Tajambula ndiwo za 1500 ndione
Him: π
Zonke Madnessπ₯
Chi nyimbo ichichi π₯π₯π₯π₯ Ka-Sir Blanca Genah Chargie ulemu wako
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Area 23
Lilongwe