YOUTH ALERT
Youth Alert! is a fun-packed trusted source of information for the youth on s*x, relationships and contraception.
we air on
Mzati FM (Mondays 4pm - 4:30pm)
YONECO (Wednesdays 4:30pm - 5pm)
ZBS & Chirundu FM (Fridays 4:30pm - 5:00m) This page is sponsored by Family Health Services (FHS) with funding from the German Development Bank through KFW; the UK government through Foreign and Commonwealth Development Office (FCDO). Views expressed in posts and comments on this page do not reflect the comments and views of the donors.
Thank you Madolo 50K followers Mbamambande
25/08/2026
๐จ๐ฅ HOOOOLAAA! WHAT IT DOOO?! ๐ค๐ฅ 50,000 AAAAA! ๐๐ฏ
Tafika pa 50K!!! 50,000 FOLLOWERS! ๐ฃ๏ธ๐ฅ๐ฅ
Kuyambira ma pen pushers โ๐พ, ma block runners ๐๐พโโ๏ธ๐จ, ma comment warriors ๐ฌ, ma silent watchers ๐, mpaka ma OG omwe mwakhala nafe kuyambira kale โ MWAPANGA IZI NAFE! ๐ซต๐พโค๏ธโ๐ฅ
Mumakonda ma post athu โค๏ธ
Mumagawana ๐
Muma commenta ๐ฌ
Muma panga tag anzanu ๐๐พ
Ndipo nthawi zonse MUMATIPEZA! ๐ฅ๐ฅ
50K si nambala yokha ayi!
Ndi mawu 50,000.
Ndi ma vibe 50,000.
Ndi maloto 50,000.
Ndi anthu 50,000 omwe akuyenda nafe pa ulendowu! ๐๐
Tikufuna kunena kuti ZIKOMO KWAMBIRI! ๐๐พโค๏ธ
Tikupanga tokha? Ayi! TIKUPANGA LIMODZI! ๐ค๐พ๐ฅ
Koma dikiraniโฆ 50K? ๐ฎโ๐จ
Iyi ndi warm-up yokha! ๐ค๐
HOLA WHAT IT DOOO?! ๐ฅ๐ฅ
50K CREW, MUKULI KUTI?! ๐ข๐ฅ
TIKUPITIRIZA! TIKUKULA! TIKUPANGA PHOKOSO! ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
25/08/2026
๐จ๐ฅ HOOOOLAAA! WHAT IT DOOO?! ๐ค๐ฅ 50,000 AAAAA! ๐๐ฏ
Tafika pa 50K!!! 50,000 FOLLOWERS! ๐ฃ๏ธ๐ฅ๐ฅ
Kuyambira ma pen pushers โ๐พ, ma block runners ๐๐พโโ๏ธ๐จ, ma comment warriors ๐ฌ, ma silent watchers ๐, mpaka ma OG omwe mwakhala nafe kuyambira kale MWAPANGA IZI NAFE! ๐ซต๐พโค๏ธโ๐ฅ
Mumakonda ma post athu โค๏ธ
Mumagawana ๐
Muma commenta ๐ฌ
Muma pangatag anzanu ๐๐พ
Ndipo nthawi zonse MUMATIPEZA! ๐ฅ๐ฅ
50K si nambala yokha ayi!
Ndi mawu 50,000.
Ndi ma vibe 50,000.
Ndi maloto 50,000.
Ndi anthu 50,000 omwe akuyenda nafe pa ulendowu! ๐๐
Tikufuna kunena kuti ZIKOMO KWAMBIRI! ๐๐พโค๏ธ
Tikupanga tokha? Ayi! TIKUPANGA LIMODZI! ๐ค๐พ๐ฅ
Koma dikiraniโฆ 50K? ๐ฎโ๐จ
Iyi ndi warm-up yokha! ๐ค๐
HOLA WHAT IT DOOO?! ๐ฅ๐ฅ
50K CREW, MUKULI KUTI?! ๐ข๐ฅ
TIKUPITIRIZA! TIKUKULA! TIKUPANGA PHOKOSO! ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
Social media ndi bwenzi kapena mdani?
Chiyambi Youth Club yatiuza momwe tingasinthire ma scroll athu kukhala learning, connections & opportunities!
Tiyeni tigwiritse ntchito social media kuti itikwezere, osati kungotitenga nthawi!
๐จ UTHENGA KAPENA ZABODZA? ๐๐ฑ
Pa social media, nkhani imafalikira mwachangu kuposa mmene timaganizira! ๐ณ Komaโฆ kodi zonse zomwe ukuwona ndi zoona?
๐๏ธ Mlambe Youth Organisation anakambako za misinformation, mmene imafalikira komanso chifukwa chake tiyenera kuganiza kaye tisanangokhulupirira kapena kugawana.
๐ Usamangodina โShareโ โ FUFUZA kaye!
โถ๏ธ Onerani clip. Ganizirani. Dziwani zoona.
Full Podcast on our Page YOUTH ALERT
Kapeni Youth Club akuti: โTikapatsidwa stage, timangotiโฆ tiyeni tiphulike!โ ๐๐ฅ
Pa sewero lawo, achinyamata awonetsa luso lawo komanso uthenga wofunika wa social Media๐ฑ๐ญ
Ndiye ngati Youth Alert yabwera kwanuโฆ MUSANGOWONERA! ๐
Bwera ndi talent yako, luso lako, mawu ako ndi creativity yako! ๐ฅ
๐ค Kuimba?
๐ Kuvina?
๐ญ Acting?
๐จ Creativity?
๐๏ธ Spoken word?
SHOW UP. STEP UP. BUST OUT YOUR TALENT! ๐ฅ๐
Kapeni Youth Club, mwachitapo bwino! ๐๐พโค๏ธ
Nanga inu, talent yanu ndi iti? ๐๐พ
13/08/2026
Basitu pheee, kwa Kabudula chills ndi madolo anzathu.
12/08/2026
Ulendoooo Ku finals congratulations scorchers chi Teamu mbambande
12/08/2026
Happy International Youth Day Madolo.....Miyoyo Yosiyana. Maloto Amodzi. (Different Contexts, Common Aspirations)
Kaya uli ku Lilongwe, Mzuzu, Blantyre, Mangochi kapena kumudzi kwanu achinyamata timakumana ndi zinthu zosiyanasiyana.
Koma pali zinthu zomwe tonse timazifuna. โค๏ธ
๐ Maphunziro abwino
๐ผ Ntchito ndi mwayi wopeza ndalama
๐ฑ Luso la zamakono ndi AI
๐ฃ๏ธ Kuti mawu athu amvedwe
๐ฑ Tsogolo labwino komanso lokhazikika
Mavuto athu akhoza kukhala osiyana, koma maloto athu ambiri ndi ofanana.
๐ฌ Question Time :
Ngati utapatsidwa mwayi wosintha Chinthu Chimodzi chokhudza moyo wa achinyamata ku Malawi, ungasinthe chiyani, ndipo chifukwa chiyani?
Tiuze maganizo ako mu comments. ๐๐พ
Chikondi cha pa Facebook chinamusintha moyo wake... koma osati mmene ankaganizira ๐๐ฑ Simudzakhulupirira zomwe zinachitikira mnzathuyu... Wotsgoinioni
Full Video on our page
Click here to claim your Sponsored Listing.
Contact the business
Telephone
Website
Address
Family Health Services (FHS)/
Lilongwe
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when YOUTH ALERT posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.