Keli P

Keli P

Share

23/06/2026

QUEST MW and Mash atulutsa album yawo now
Is available everywhere

πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

22/06/2026

Amkulu Awa eeeh chonena ndilibe
Inuyo ngati muli ndi mau tiyeni ku ma comments⚽

22/06/2026

Inu Amvekele mkazi akadzangokuuzani kuti ndi wachikonda muzangodziwa kuti chikondi anagwila kale πŸ˜‚
Iyi yokha yabayaπŸ˜…

22/06/2026

75K followersβ€οΈπŸ¦… Ulemu wanu fam.

22/06/2026

🌹Vibe on vibe

21/06/2026

Ma guys ngati muli ndi mau ndiyakhuleni ndisanagone

21/06/2026

Mamawa uno chimwemwe changa nchoti fanzi yanga ikuvela nyimbo zaine ku audiomark I love you guys Manja mwanu πŸ‘ ndi makudalilani
nthawi zonse πŸ”₯πŸ‡²πŸ‡ΌπŸ™

20/06/2026

Musanagone kaveleni ep yanga ku audiomark fam
πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯πŸ”₯

20/06/2026

Nde mwati mpira ukuyenda bwino koma??
Tikakhala ife a Brazil πŸ‡§πŸ‡· tawinaπŸ˜€

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Luchenza?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Address


Luchenza