STRAS WORLD

STRAS  WORLD

Share

World of fun and enjoyment

04/03/2026

TOASTT wa dropper diss to IKK kuseliku 🎵🔥

04/03/2026

Akuti iye sangamavale ma Skin jeans ngati anyamata a Chamba aku America..

‎Mayhoo anyozeka!!!

‎Mu interview Ina mkuluyi walankhula kuti akuti iyeyo ndi mamuna odziwa kutchena Asia Yonse.

‎Kim Jong Un, wanena kuti nthawi zambiri mkazi wake amamuyamikila kuti iyeyo amatchena kuponsa aliense ku Asia. "My wife says I am the most fashionable man in Asia"

‎"Izi zimandichititsa kukhala okondwa, ndimadziwa kuti anthu amakulemekeza ndi momwe ukuonekela. Ndiine m'tsogoleri wadziko lamphanvu, lotamika padziko lonse lapansi, osayembekezela kuti ndingavale tima skin jeans ngati anyamata aku Western, omwe amakamba zamisala mu nyimbo zawo. Ma trouser omwe ndimavala amayimila ulemu komanso ulamuliro." Adamaliza choncho m'tsogoleriyo...

02/03/2026

Munapangapo izi I know 🌎

02/03/2026

blessed y'all 🌎

02/03/2026

sole north Korea ain't nobody wants your toys yet 🤣

01/03/2026

Guys timve nawo mawu
Mutu;verse lake BC 🙏

01/03/2026

Top Fans, we value your feedback and would like to know what you would like to see from us this week. Should we feature music, stories, reels, or trending topics? The most popular comment will determine our content strategy. Mso Pah

Photos from STRAS  WORLD's post 01/03/2026

Njuchi is back 🔥🔥🔥

25/02/2026

You shall change the game 🎯

24/02/2026

LISTEN the Stras

22/02/2026

Sunday lero tatiyeni timve mau achilimbikitso APA 🙏🙏🙏🙏

Want your business to be the top-listed Media Company in Mzimba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Mzimba