Timaphusha Talent
π¨TIPHUSHE LUSO From GHETTO to the World π MUSIC, MODELING, DANCING and so many ARTS ππ
18/08/2026
π― TAKE ME BACK TUESDAY βΌοΈπ
π£οΈ Nthawi imeneyi Ma Artist Awa ankayatsa moto kwambiri Mu ghettoπ₯π₯ .... Malinga Mafia Ndyemwe akuipsabe Moto mpaka pano...
π£οΈ Madala ....pano anazizila kwambiri.. Za music kuli zii mwina anapanga RETIRE π€·πΎββοΈπ
βΌοΈNepia chipitileni ku AMERICA πΊπΈ kuja anatulutsa ALBUM last Year koma pano naye kuli zii.... Komano Zili bwino fukwa moyo wake ukuyenda bhoo.. AKanakhala ku Malawi bwenzi Angokanda mu NDIRANDE mu ππππΎπ₯³
18/08/2026
π THROWBACK βΌοΈ π³
π£οΈ Photo iyi anajambula mu nyimbo yanji yot muli and πΏπ¦ π ππ₯π₯
π£οΈ Tione amene Amasata SA HIP-HOP πΏπ¦π₯π₯ππΎ
18/08/2026
π TRENDING βΌοΈ π³
π£οΈ Pamene nkaz yo amazazindikila k*t Si MADNESS uyu Chinali k*t Chazepulq kale Atatu iiih π π π π π Koma Tint uyu ππΎππΎπππ
π£οΈ Subscribe ππΎπ€πΎ
https://www.youtube.com/-vc4qh
17/08/2026
π Anthu ak*ti bwanj za NYIMBO YA ICHII ( JOE IKON) iyi ak*ti YOTENTHA π³π³π²πΌπ₯π―π€£π
17/08/2026
π G aka KING π KATAKWE nd TOP FAN ππ²πΌπ― π₯ kogulitsa merchandise ya A'BA'LE π OKHA π₯ππΎπ
17/08/2026
π TRENDING βΌοΈ π³
π£οΈ Chinthuzi izi chinajambulidwa mu nyimbo yanj π€π€π²πΌ tione yemwe Amasata MALAWI π²πΌ URBAN MUSIC ππ₯π₯
17/08/2026
π SHOUT out TO BERNADETTA uyu nde wasewera so bwino kwambiri WAFCON ija nd SCORCHERS π²πΌπ π₯π₯π₯
17/08/2026
π HAPPY BIRTHDAY TO GUN BOSS... Malinga Mafia ππππ
π£οΈ MALAWI π²πΌ DANCEHALL ICON and Top Shatta πππΎπΎπΎ
10/08/2026
π TRENDING MAGANIZO βΌοΈ π³
π£οΈ Anthu ambiri ak*ti a FAM β½ π²πΌπ akanapanga chotheka k*t apite ku MOROCCO π²π¦ akayipase moto SCORCHERS π²πΌ π kuma STAND kuja eti bwaa π π ππΎ
βΌοΈ Inu muona bwaa π³ Apitedi or Ayii π³ππ
10/08/2026
π THROWBACK βΌοΈ π³
π£οΈ PANO KIZITO Mene Ali nd Chokwera π ma BADDIE akamuona moyenda mu akumamuyang'ana CHONCHI ngat mene anapangila apaππππΎ
Ichi chinasintha LEVEL kwambiri even body inasintha nawo eeh Mdalitso nd Ntendele kwa KIZITO Dolo ka Fafandede Sauzande ππΎ ππππΎππ²πΌβ¨ SUPERSTAR β¨
π staring at KIZITO ku COSOMA Conference MANGOCHI π₯π²πΌ
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
City Centre
Zomba
Alerts
Be the first to know and let us send you an email when Timaphusha Talent posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.